1 Mafumu 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo anapitiriza kuchita ngati aneneri+ mpaka dzuwa linapendeka. Anapitirizabe mpaka nthawi yopereka nsembe yambewu, koma sipanamveke mawu alionse. Palibe anawayankha kapena kuwamvera.+
29 Iwo anapitiriza kuchita ngati aneneri+ mpaka dzuwa linapendeka. Anapitirizabe mpaka nthawi yopereka nsembe yambewu, koma sipanamveke mawu alionse. Palibe anawayankha kapena kuwamvera.+