1 Mafumu 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho Eliya anatenga miyala 12 mogwirizana ndi chiwerengero cha mafuko a ana a Yakobo, yemwe mawu a Yehova anam’fikira,+ akuti: “Dzina lako lidzakhala Isiraeli.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:31 Tsanzirani, ptsa. 88-90 Nsanja ya Olonda,1/1/2008, tsa. 20
31 Choncho Eliya anatenga miyala 12 mogwirizana ndi chiwerengero cha mafuko a ana a Yakobo, yemwe mawu a Yehova anam’fikira,+ akuti: “Dzina lako lidzakhala Isiraeli.”+