-
1 Mafumu 18:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Kenako iye anati: “Thiraninso madzi ena.” Anthuwo anathiranso. Ndiyeno Eliya anati: “Thiraninso kachitatu.” Choncho anthuwo anathiranso kachitatu.
-