1 Mafumu 18:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Atatero, moto+ wa Yehova unatsika n’kunyeketsa nsembe yopsereza+ ija, nkhuni, miyala ndi fumbi lomwe. Unaumitsanso madzi amene anali m’ngalande muja.+
38 Atatero, moto+ wa Yehova unatsika n’kunyeketsa nsembe yopsereza+ ija, nkhuni, miyala ndi fumbi lomwe. Unaumitsanso madzi amene anali m’ngalande muja.+