1 Mafumu 18:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kenako anauza mtumiki wake kuti: “Pita ukayang’ane mbali ya kunyanja.” Mtumikiyo anapita n’kukayang’anadi, ndiyeno anati: “Kulibe kalikonse.” Koma Eliya anamubweza n’kumuuza kuti, “Pita ukayang’anenso.” Anachita zimenezi mpaka maulendo 7.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:43 Tsanzirani, ptsa. 94-95 Nsanja ya Olonda,4/1/2008, ptsa. 18-19
43 Kenako anauza mtumiki wake kuti: “Pita ukayang’ane mbali ya kunyanja.” Mtumikiyo anapita n’kukayang’anadi, ndiyeno anati: “Kulibe kalikonse.” Koma Eliya anamubweza n’kumuuza kuti, “Pita ukayang’anenso.” Anachita zimenezi mpaka maulendo 7.+