1 Mafumu 18:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pa nthawiyo kumwamba kunachita mdima wa mitambo ndipo kunja kunawomba mphepo.+ Kenako kunayamba kugwa chimvula chambiri.+ Ahabu anali akuyenda pagaleta mpaka anakafika ku Yezereeli.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:45 Tsanzirani, tsa. 97 Nsanja ya Olonda,4/1/2008, tsa. 20
45 Pa nthawiyo kumwamba kunachita mdima wa mitambo ndipo kunja kunawomba mphepo.+ Kenako kunayamba kugwa chimvula chambiri.+ Ahabu anali akuyenda pagaleta mpaka anakafika ku Yezereeli.+