1 Mafumu 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Ahabu+ anauza Yezebeli+ zonse zimene Eliya anachita, ndiponso mmene anaphera aneneri onse ndi lupanga.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:1 Tsanzirani, tsa. 101 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, ptsa. 18-19
19 Kenako Ahabu+ anauza Yezebeli+ zonse zimene Eliya anachita, ndiponso mmene anaphera aneneri onse ndi lupanga.+