1 Mafumu 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Eliya anachita mantha moti ananyamuka n’kuyamba kuthawa kuti apulumutse moyo wake,+ mpaka anakafika ku Beere-seba+ wa ku Yuda.+ Mtumiki wake anamusiya kumeneko, 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:3 Tsanzirani, ptsa. 101-102 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, ptsa. 19-20
3 Choncho Eliya anachita mantha moti ananyamuka n’kuyamba kuthawa kuti apulumutse moyo wake,+ mpaka anakafika ku Beere-seba+ wa ku Yuda.+ Mtumiki wake anamusiya kumeneko,