1 Mafumu 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Patapita kanthawi, mngelo+ wa Yehova uja anabweranso kachiwiri n’kumukhudza, ndipo anamuuza kuti: “Dzuka udye, popeza ulendowu wakukulira.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:7 Tsanzirani, tsa. 103 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, tsa. 20
7 Patapita kanthawi, mngelo+ wa Yehova uja anabweranso kachiwiri n’kumukhudza, ndipo anamuuza kuti: “Dzuka udye, popeza ulendowu wakukulira.”+