10 Iye anayankha kuti: “Ndachitira nsanje kwambiri+ inu Yehova Mulungu wa makamu, chifukwa ana a Isiraeli asiya pangano lanu.+ Agwetsa maguwa anu ansembe,+ ndipo apha aneneri anu ndi lupanga,+ moti ine ndatsala ndekhandekha.+ Tsopano ayambanso kundifunafuna kuti achotse moyo wanga.”+