1 Mafumu 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ine ndasiya anthu 7,000 mu Isiraeli,+ amene mawondo awo sanagwadirepo Baala,+ ndiponso pakamwa pawo sipanapsompsonepo Baala.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:18 Tsanzirani, tsa. 107 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, tsa. 22
18 Ine ndasiya anthu 7,000 mu Isiraeli,+ amene mawondo awo sanagwadirepo Baala,+ ndiponso pakamwa pawo sipanapsompsonepo Baala.”+