1 Mafumu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho anabwerera n’kutenga ng’ombe zamphongo ziwiri n’kuzipha.*+ Anatenga mitengo ya pulawo+ ya ng’ombezo n’kuphikira nyama yake. Kenako anaipereka kwa anthu kuti adye. Atatero, iye ananyamuka n’kutsatira Eliya ndipo anayamba kum’tumikira.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:21 Nsanja ya Olonda,11/1/1997, ptsa. 30-31
21 Choncho anabwerera n’kutenga ng’ombe zamphongo ziwiri n’kuzipha.*+ Anatenga mitengo ya pulawo+ ya ng’ombezo n’kuphikira nyama yake. Kenako anaipereka kwa anthu kuti adye. Atatero, iye ananyamuka n’kutsatira Eliya ndipo anayamba kum’tumikira.+