2 Mafumu 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mfumu ya Yuda imene yakutumani kuti mudzafunse kwa Yehova, mukaiuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ponena za mawu amene wamvawo,+
18 Mfumu ya Yuda imene yakutumani kuti mudzafunse kwa Yehova, mukaiuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ponena za mawu amene wamvawo,+