2 Mafumu 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “N’chifukwa chake ndidzakugoneka+ pamodzi ndi makolo ako, ndipo ndithu udzaikidwa m’manda ako mu mtendere.+ Maso ako sadzaona tsoka lonse limene ndikulibweretsa pamalo ano.”’” Choncho iwo anabweretsa mawuwo kwa mfumuyo. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:20 Nsanja ya Olonda,12/15/2000, tsa. 309/15/2000, tsa. 30
20 “N’chifukwa chake ndidzakugoneka+ pamodzi ndi makolo ako, ndipo ndithu udzaikidwa m’manda ako mu mtendere.+ Maso ako sadzaona tsoka lonse limene ndikulibweretsa pamalo ano.”’” Choncho iwo anabweretsa mawuwo kwa mfumuyo.