2 Mafumu 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wina akudula mtengo, nkhwangwa yake inaguluka+ n’kugwera m’madzi. Pamenepo munthuyo anayamba kulira kuti: “Kalanga ine mbuyanga!+ Nkhwangwayo inali yobwereka!”+
5 Munthu wina akudula mtengo, nkhwangwa yake inaguluka+ n’kugwera m’madzi. Pamenepo munthuyo anayamba kulira kuti: “Kalanga ine mbuyanga!+ Nkhwangwayo inali yobwereka!”+