2 Mafumu 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano mfumu ya Siriya+ inayamba kuchita nkhondo ndi Isiraeli. Chotero inakambirana ndi atumiki ake+ kuti: “Tikasonkhane pamalo akutiakuti.”+
8 Tsopano mfumu ya Siriya+ inayamba kuchita nkhondo ndi Isiraeli. Chotero inakambirana ndi atumiki ake+ kuti: “Tikasonkhane pamalo akutiakuti.”+