2 Mafumu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nthawi yomweyo mfumuyo inatumizako mahatchi, magaleta ankhondo, ndi gulu lalikulu la asilikali amphamvu.+ Iwo anafikako usiku ndipo anazungulira mzindawo.
14 Nthawi yomweyo mfumuyo inatumizako mahatchi, magaleta ankhondo, ndi gulu lalikulu la asilikali amphamvu.+ Iwo anafikako usiku ndipo anazungulira mzindawo.