2 Mafumu 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atangofika ku Samariya, Elisa anati: “Yehova, atseguleni maso anthuwa kuti aone.” Nthawi yomweyo Yehova anatsegula maso awo ndipo anaona+ kuti ali pakatikati pa Samariya.
20 Atangofika ku Samariya, Elisa anati: “Yehova, atseguleni maso anthuwa kuti aone.” Nthawi yomweyo Yehova anatsegula maso awo ndipo anaona+ kuti ali pakatikati pa Samariya.