1 Mbiri 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amenewa ndiwo anali ana onse a Davide, kuwonjezera pa ana a adzakazi ake, ndipo Tamara+ anali mlongo wawo.
9 Amenewa ndiwo anali ana onse a Davide, kuwonjezera pa ana a adzakazi ake, ndipo Tamara+ anali mlongo wawo.