1 Mbiri 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Onsewa anali ana a Yediyaeli, atsogoleri a nyumba ya makolo awo. Anali amuna 17,200, amuna amphamvu ndi olimba mtima,+ opita ku nkhondo.
11 Onsewa anali ana a Yediyaeli, atsogoleri a nyumba ya makolo awo. Anali amuna 17,200, amuna amphamvu ndi olimba mtima,+ opita ku nkhondo.