1 Mbiri 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Bambo wawo Efuraimu anawalira kwa masiku ambiri,+ ndipo abale ake ankabwera kudzam’tonthoza.