1 Mbiri 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Elipaala anaberekanso Beriya ndi Sema. Amenewa anali atsogoleri a nyumba za makolo a anthu okhala ku Aijaloni.+ Iwo ndiwo anathamangitsa anthu a ku Gati.
13 Elipaala anaberekanso Beriya ndi Sema. Amenewa anali atsogoleri a nyumba za makolo a anthu okhala ku Aijaloni.+ Iwo ndiwo anathamangitsa anthu a ku Gati.