2 Mbiri 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nyumba yaikuluyo anaikuta+ ndi matabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza, kenako anaikutanso ndi golide wabwino.+ Atatero, anaikongoletsa ndi zithunzi za mitengo yakanjedza+ zojambula mochita kugoba ndiponso matcheni.+
5 Nyumba yaikuluyo anaikuta+ ndi matabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza, kenako anaikutanso ndi golide wabwino.+ Atatero, anaikongoletsa ndi zithunzi za mitengo yakanjedza+ zojambula mochita kugoba ndiponso matcheni.+