2 Mbiri 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika m’mapiri ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe atsogoleri.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake mu mtendere.’”+
16 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika m’mapiri ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe atsogoleri.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake mu mtendere.’”+