2 Mbiri 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehoramu anali ndi zaka 32 pamene anayamba kulamulira ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 8. Pomalizira pake iye anapita popanda womumvera chisoni.+ Choncho anamuika m’manda mu Mzinda wa Davide,+ koma osati m’manda a mafumu.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:20 Nsanja ya Olonda,11/15/1998, tsa. 32
20 Yehoramu anali ndi zaka 32 pamene anayamba kulamulira ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 8. Pomalizira pake iye anapita popanda womumvera chisoni.+ Choncho anamuika m’manda mu Mzinda wa Davide,+ koma osati m’manda a mafumu.+