2 Mbiri 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Gawo limodzi mwa magawo atatu lidzakhale panyumba ya mfumu,+ ndipo gawo lina limodzi mwa magawo atatu a inu lidzakhale pachipata chotchedwa Maziko.+ Anthu onse adzakhale pamabwalo+ a nyumba ya Yehova.
5 Gawo limodzi mwa magawo atatu lidzakhale panyumba ya mfumu,+ ndipo gawo lina limodzi mwa magawo atatu a inu lidzakhale pachipata chotchedwa Maziko.+ Anthu onse adzakhale pamabwalo+ a nyumba ya Yehova.