2 Mbiri 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ataliya atamva anthu akuchita phokoso komanso akuthamanga ndi kutamanda mfumu,+ nthawi yomweyo anapita kwa anthu amene anali panyumba ya Yehova.
12 Ataliya atamva anthu akuchita phokoso komanso akuthamanga ndi kutamanda mfumu,+ nthawi yomweyo anapita kwa anthu amene anali panyumba ya Yehova.