2 Mbiri 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anam’gwira n’kutuluka naye. Atangofika pakhomo la kunyumba ya mfumu lolowera mahatchi, anam’phera pomwepo.+
15 Choncho anam’gwira n’kutuluka naye. Atangofika pakhomo la kunyumba ya mfumu lolowera mahatchi, anam’phera pomwepo.+