2 Mbiri 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehoasi anali ndi zaka 7 pamene anayamba kulamulira.+ Iye analamulira zaka 40 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Beere-seba+ ndipo dzina lawo linali Zibiya.
24 Yehoasi anali ndi zaka 7 pamene anayamba kulamulira.+ Iye analamulira zaka 40 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Beere-seba+ ndipo dzina lawo linali Zibiya.