2 Mbiri 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pajatu ana+ a Ataliya mkazi woipa uja anathyola nyumba ya Mulungu woona,+ n’kutenga zinthu zonse zopatulika+ za m’nyumba ya Yehovayo n’kukazipereka kwa Abaala.”+
7 Pajatu ana+ a Ataliya mkazi woipa uja anathyola nyumba ya Mulungu woona,+ n’kutenga zinthu zonse zopatulika+ za m’nyumba ya Yehovayo n’kukazipereka kwa Abaala.”+