2 Mbiri 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatero anauza anthu onse a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho wopatulika+ umene Mose+ mtumiki wa Mulungu woona analamula Aisiraeli m’chipululu.
9 Atatero anauza anthu onse a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho wopatulika+ umene Mose+ mtumiki wa Mulungu woona analamula Aisiraeli m’chipululu.