2 Mbiri 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anapitiriza kutumiza aneneri+ pakati pawo kuti awabwezere kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kupereka umboni wowatsutsa, koma sanamvere.+
19 Yehova anapitiriza kutumiza aneneri+ pakati pawo kuti awabwezere kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kupereka umboni wowatsutsa, koma sanamvere.+