2 Mbiri 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mfumu Yehoasi sanakumbukire kukoma mtima kosatha kumene Yehoyada bambo a Zekariya anamusonyeza,+ ndipo anapha mwana wawo yemwe pakufa ananena kuti: “Yehova aone zimene mwachitazi ndi kubwezera.”+
22 Mfumu Yehoasi sanakumbukire kukoma mtima kosatha kumene Yehoyada bambo a Zekariya anamusonyeza,+ ndipo anapha mwana wawo yemwe pakufa ananena kuti: “Yehova aone zimene mwachitazi ndi kubwezera.”+