2 Mbiri 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Yotamu anapitiriza kulimbitsa ufumu wake, popeza anakonza njira zake pamaso pa Yehova Mulungu wake.+
6 Chotero Yotamu anapitiriza kulimbitsa ufumu wake, popeza anakonza njira zake pamaso pa Yehova Mulungu wake.+