Ezara 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu onse okhala nawo pafupi anawathandiza*+ powapatsa ziwiya zasiliva, golide, katundu, ziweto, ndi zinthu zabwinozabwino, kuwonjezera pa zonse zimene zinaperekedwa mwaufulu.+
6 Anthu onse okhala nawo pafupi anawathandiza*+ powapatsa ziwiya zasiliva, golide, katundu, ziweto, ndi zinthu zabwinozabwino, kuwonjezera pa zonse zimene zinaperekedwa mwaufulu.+