-
Ezara 1:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ziwiyazo zinali zochuluka chonchi: ziwiya 30 zagolide zooneka ngati mabasiketi, ziwiya 1,000 zasiliva zooneka ngati mabasiketi, ndi ziwiya 29 zowonjezera.
-