Ezara 2:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Mogwirizana ndi chuma chawo, anapereka golide+ kuti athandize pa ntchitoyo wokwana madalakima* 61,000, siliva+ wokwana ma mina* 5,000 ndi mikanjo 100+ ya ansembe.
69 Mogwirizana ndi chuma chawo, anapereka golide+ kuti athandize pa ntchitoyo wokwana madalakima* 61,000, siliva+ wokwana ma mina* 5,000 ndi mikanjo 100+ ya ansembe.