Nehemiya 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno tsiku lina m’mwezi wa Nisani,*+ m’chaka cha 20+ cha mfumu Aritasasita,+ mfumuyo inali kufuna vinyo. Pamenepo ine ndinatenga vinyoyo ndi kum’pereka kwa mfumu monga mwa nthawi zonse.+ Koma ndinali ndisanakhalepo wachisoni pamaso pake.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, ptsa. 8-910/15/1990, ptsa. 10-111/15/1986, tsa. 7 Ulosi wa Danieli, tsa. 197
2 Ndiyeno tsiku lina m’mwezi wa Nisani,*+ m’chaka cha 20+ cha mfumu Aritasasita,+ mfumuyo inali kufuna vinyo. Pamenepo ine ndinatenga vinyoyo ndi kum’pereka kwa mfumu monga mwa nthawi zonse.+ Koma ndinali ndisanakhalepo wachisoni pamaso pake.+
2:1 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, ptsa. 8-910/15/1990, ptsa. 10-111/15/1986, tsa. 7 Ulosi wa Danieli, tsa. 197