Nehemiya 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno mfumu inati: “N’chifukwa chiyani nkhope yako ili yachisoni+ pamene sukudwala? Pali chinachake chimene chikukuvutitsa mumtima.”+ Atanena zimenezi ndinachita mantha kwambiri.
2 Ndiyeno mfumu inati: “N’chifukwa chiyani nkhope yako ili yachisoni+ pamene sukudwala? Pali chinachake chimene chikukuvutitsa mumtima.”+ Atanena zimenezi ndinachita mantha kwambiri.