Nehemiya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mfumu inandiyankha kuti: “Ulendo wako udzatenga masiku angati, ndipo udzabwera liti?” Pa nthawiyi, mkazi wamkulu wa mfumu anali atakhala pambali pake. Choncho mfumu inandilola kupita nditaiuza nthawi.+
6 Mfumu inandiyankha kuti: “Ulendo wako udzatenga masiku angati, ndipo udzabwera liti?” Pa nthawiyi, mkazi wamkulu wa mfumu anali atakhala pambali pake. Choncho mfumu inandilola kupita nditaiuza nthawi.+