Nehemiya 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinayendabe mpaka kukafika ku Chipata cha Kukasupe+ ndi ku Dziwe la Mfumu, ndipo kumeneko kunalibe njira imene chiweto chimene ndinakwerapo chikanadutsa.
14 Ndinayendabe mpaka kukafika ku Chipata cha Kukasupe+ ndi ku Dziwe la Mfumu, ndipo kumeneko kunalibe njira imene chiweto chimene ndinakwerapo chikanadutsa.