Nehemiya 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma usikuwo ndinayendabe mokwezeka m’chigwamo+ ndipo ndinapitirizabe kuonetsetsa mpandawo. Kenako ndinabwerera ndi kukalowanso pa Chipata cha Kuchigwa.+
15 Koma usikuwo ndinayendabe mokwezeka m’chigwamo+ ndipo ndinapitirizabe kuonetsetsa mpandawo. Kenako ndinabwerera ndi kukalowanso pa Chipata cha Kuchigwa.+