Nehemiya 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atsogoleri+ a kumeneko sanadziwe kumene ndapita ndi zimene ndinali kuchita. Komanso Ayuda pamodzi ndi ansembe, anthu olemekezeka, atsogoleri ndi ena onse amene akanagwira ntchito yomanga mpanda ndinali ndisanawauze kalikonse.
16 Atsogoleri+ a kumeneko sanadziwe kumene ndapita ndi zimene ndinali kuchita. Komanso Ayuda pamodzi ndi ansembe, anthu olemekezeka, atsogoleri ndi ena onse amene akanagwira ntchito yomanga mpanda ndinali ndisanawauze kalikonse.