Nehemiya 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamapeto pake ndinawauza kuti: “Inu mukuona vuto lalikulu limene tili nalo. Mukuona kuti Yerusalemu ali bwinja ndipo zipata zake zinatenthedwa ndi moto. Tiyeni timange mpanda wa Yerusalemu kuti anthu asiye kutitonza.”+
17 Pamapeto pake ndinawauza kuti: “Inu mukuona vuto lalikulu limene tili nalo. Mukuona kuti Yerusalemu ali bwinja ndipo zipata zake zinatenthedwa ndi moto. Tiyeni timange mpanda wa Yerusalemu kuti anthu asiye kutitonza.”+