Nehemiya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Sanibalati+ wa ku Beti-horoni, Tobia+ mtumiki+ wachiamoni+ ndi Gesemu+ Mluya+ atamva zimenezi anayamba kutinyoza+ ndi kutiyang’ana moipidwa. Iwo anati: “N’chiyani chimene mukuchitachi? Kodi mukupandukira mfumu?”+
19 Ndiyeno Sanibalati+ wa ku Beti-horoni, Tobia+ mtumiki+ wachiamoni+ ndi Gesemu+ Mluya+ atamva zimenezi anayamba kutinyoza+ ndi kutiyang’ana moipidwa. Iwo anati: “N’chiyani chimene mukuchitachi? Kodi mukupandukira mfumu?”+