-
Nehemiya 3:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako Refaya mwana wamwamuna wa Hura, kalonga wa hafu ya chigawo cha Yerusalemu, anakonza mpandawo kuchokera pamene Hananiya analekezera.
-