Nehemiya 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Hananiya mwana wamwamuna wa Selemiya ndi Hanuni mwana wamwamuna wa 6 wa Zalafi, anakonzanso chigawo china cha mpanda. Kenako Mesulamu+ mwana wamwamuna wa Berekiya, anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba* yake kuchokera pamene winayo analekezera.+
30 Hananiya mwana wamwamuna wa Selemiya ndi Hanuni mwana wamwamuna wa 6 wa Zalafi, anakonzanso chigawo china cha mpanda. Kenako Mesulamu+ mwana wamwamuna wa Berekiya, anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba* yake kuchokera pamene winayo analekezera.+