Nehemiya 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiponso ine, abale anga ndi atumiki anga, tikukongoza ndalama ndi chakudya kwa abale athu. Chonde, tiyeni tileke kulandira chiwongoladzanja tikakongoza zinthu.+
10 Ndiponso ine, abale anga ndi atumiki anga, tikukongoza ndalama ndi chakudya kwa abale athu. Chonde, tiyeni tileke kulandira chiwongoladzanja tikakongoza zinthu.+