Nehemiya 7:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Ansembe+ anali awa: ana a Habaya, ana a Hakozi+ ana a Barizilai+ amene anatenga mkazi pakati pa ana aakazi a Barizilai+ Mgiliyadi ndipo anayamba kutchedwa ndi dzina lawo.
63 Ansembe+ anali awa: ana a Habaya, ana a Hakozi+ ana a Barizilai+ amene anatenga mkazi pakati pa ana aakazi a Barizilai+ Mgiliyadi ndipo anayamba kutchedwa ndi dzina lawo.