Esitere 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha.